Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 9:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pamene Mose adalankhulira anthu once lamulo liri lonse monga mwa cilamulo, anatenga mwazi wa ana a ng'ombe ndi mbuzi, pamodzi ndi madzi ndi ubweya wofiira ndi hisope, nawaza buku lomwe, ndi anthu onse,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 9

Onani Ahebri 9:19 nkhani