Pakuti powachulira iwo cifukwa, anena,Taonani, akudza masiku, anena Ambuye,Ndipo ndidzapangana pangano latsopano ndi nyumba ya Israyeli, ndi nyumba ya Yuda,