Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 7:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti cilamulo cimaika akuru a ansembe anthu, okhala naco cifoko; koma mau a lumbirolo, amene anafika citapita cilamulo, aika Mwana, woyesedwa wopanda cirema ku nthawi zonse.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 7

Onani Ahebri 7:28 nkhani