Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ameneyo, m'masiku a thupi lace anapereka mapemphero ndi mapembedzero pamodzi ndi kulira kwakukuru ndi misozi kwa iye amene anakhoza kumpulumutsa iye muimfa, ndipo anamveka popeza anaopa Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 5

Onani Ahebri 5:7 nkhani