Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 5:13-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

13. Pakuti yense wakudya mkaka alibe cizolowezi ca mau a cilungamo; pakuti ali khanda.

14. Koma cakudya cotafuna ciri ca anthu akulu misinkhu, amene mwa kucita nazo anazoloweretsa zizindikiritso zao kusiyanitsa cabwino ndi coipa.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 5