Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 12:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ici, cakuti kamodzinso, cilozera kusuntha kwace kwa zinthu zogwedezeka, monga kwa zinthu zolengedwa, kuti zinthu zosagwedezeka zikhale.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 12

Onani Ahebri 12:27 nkhani