Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ahebri 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwakonda cilungamo, ndi kudana naco coipa;Mwa ici Mulungu, ndiye Mulungu wanu, wakudzozaniNdi mafuta a cikondwerero ceni ceni koposa anzanu.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 1

Onani Ahebri 1:9 nkhani