Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 6:17-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

17. Kuyambira tsopano palibe munthu andibvute, pakuti ndiri nayo ine m'thupi mwanga mikwingwirima ya Yesu.

18. Cisomo ca Ambuye wathu Yesu Kristu cikhale ndi mzimu wanu, abale. Amen.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 6