Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abale, ngatinso munthu agwidwa nako kulakwa kwakuti, inu auzimu, mubweze wotereyo mu mzimu wa cifatso; ndikudzipenyerera wekha, ungayesedwe nawenso.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 6

Onani Agalatiya 6:1 nkhani