Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 5:23-26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. cifatso, ciletso; pokana zimenezi palibe lamulo.

24. Koma iwo a Kristu Yesu adapacika thupi, ndi zokhumba zace, ndi zilakolako zace.

25. 1 N gati tiri ndi moyo ndi Mzimu, ndi Mzimunso tiyende.

26. 2 Tisakhale odzikuza, outsana, akucitirana njiru.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 5