Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndikhulupirira inu mwa Ambuye, kuti simudzakhala nao mtima wina; koma iye wakubvuta inu, angakhale ali yani, adzasenza citsutso cace.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 5

Onani Agalatiya 5:10 nkhani