Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo cija ca m'thupi langa cakukuyesani inu simunacipeputsa, kapena sicinakunyansirani, komatu munandilandira ine monga mngelo wa Mulungu, monga Kristu Yesu mwini.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 4

Onani Agalatiya 4:14 nkhani