Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 3:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. 4 Pakuti nonse amene munabatizidwa kwa Kristu mudabvala Kristu.

28. 5 Muno mulibe Myuda, kapena Mhelene, muno mulibe kapolo, kapena mfulu, muno mulibe mwamuna ndi mkazi; 6 pakuti muli nonse mmodzi mwa Kristu Yesu.

29. Koma ngati muli a Kristu, muli mbeu ya Abrahamu, 7 nyumba monga mwa Lonjezano.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 3