Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo kodi cilamulo citsutsana nao malonjezano a Mulungu? Msatero ai. Pakuti cikadapatsidwa cilamulo eakukhoza kucitira moyo, cilungamo cikadacokera ndithu kulamulo.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 3

Onani Agalatiya 3:21 nkhani