Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Agalatiya opusa inu, anakulodzani ndani, inu amene Kristu anaonetsedwa pa maso panu, wopacikidwa?

2. ici cokha ndifuna kuphunzira kwa inu, Kodi munalandira Mzimuyo ndi nchito za lamulo, kapena ndi kumva kwa cikhulupiriro?

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 3