Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ndinakwera kunkako mobvumbulutsa; ndipo ndinawauza Uthenga Wabwino umene ndiulalikira kwa amitundu; koma m'tseri kwa iwo omveka, kuti kapena ndingathamange, kapena ndikadathamanga cabe.

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 2

Onani Agalatiya 2:2 nkhani