Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Agalatiya 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu pamene ndinaona kuti sanalikuyenda koongoka, monga mwa coonadi ca Uthenga Wabwino, ndinati kwa Kefa pamaso pa onse, Ngati inu muli Myuda mutsata makhalidwe a amitundu, ndipo si a Ayuda, mukangamiza bwanji amitundu atsate makhalidwe a Ayuda?

Werengani mutu wathunthu Agalatiya 2

Onani Agalatiya 2:14 nkhani