Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cotsalira, abale, zinthu ziri zonse zoona, ziri zonse zolemekezeka, ziri zonse zolungama, ziri zonse zoyera, ziri zonse zokongola, ziri zonse zimveka zokoma; ngati kuli cokoma mtima cina, kapena citamando cina, zilingirireni izi.

Werengani mutu wathunthu Afilipi 4

Onani Afilipi 4:8 nkhani