Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 2:29-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Cifukwa cace mumlandire mwa Ambuye, ndi cimwemweconse; nimucitire ulemu oterewa;

30. pakuti cifukwa lea nchito ya Kristu anafikira pafupi imfa, wosasamalira moyo wace, kuti z akakwaniritse ciperewero ca utumiki wanu wa kwa ine.

Werengani mutu wathunthu Afilipi 2