Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero, okondedwa anga, monga momwe mumvera nthawi zonse, posati pokha pokha pokhala ine ndiripo, komatu makamaka tsopano pokhala ine palibe, gwirani nchito yace ya cipulumutso canu ndi mantha, ndi kunthunthumira;

Werengani mutu wathunthu Afilipi 2

Onani Afilipi 2:12 nkhani