Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

monga mwa kulingiriritsa ndi ciyembekezo canga, kuti palibe cinthu cidzandicititsa manyazi, komatu mwa kulimbika mtima konse, monga nthawi yonse, tsopanonso Kristu adzakuzidwa m'thupi langa, kapena mwamoyo, kapena mwa imfa.

Werengani mutu wathunthu Afilipi 1

Onani Afilipi 1:20 nkhani