Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Afilipi 1:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. PAULO ndi Timoteo, akapolo a Yesu Kristu, kwa oyera mtima onse mwa Kristu Yesu, akukhala ku Filipi, pamodzi ndi oyang'anira ndi atumiki:

2. Cisomo kwa inu ndi mtendere za kwa Mulungu Atate wathu ndi Ambuye Yesu Kristu.

Werengani mutu wathunthu Afilipi 1