Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aefeso 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo, ambuye inu, muwacitire zomwezo iwowa, nimuleke kuwaopsa; podziwa kuti Ambuye wao ndi wanu ali m'Mwamba, ndipo palibe tsankhu kwa iye.

Werengani mutu wathunthu Aefeso 6

Onani Aefeso 6:9 nkhani