Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aefeso 6:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa kuti kulimbana kwathu sitilimbana nao mwazi ndi thupi, komatu nao maukulu, ndi maulamuliro, ndi akucita zolimbika a dziko lapansi a mdima uno, ndi a uzimu a coipa m'zakumwamba.

Werengani mutu wathunthu Aefeso 6

Onani Aefeso 6:12 nkhani