Komanso inu, yense pa yekha, yense akonde mkazi wace wa iye yekha, monga adzikonda yekha; ndipo 2 mkaziyo akumbukile kuti aziopa mwamuna.