Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aefeso 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

atacotsa udani m'thupi lace, ndiwo mau a cilamulo ca kuchulako malangizo; kuti alenge awiriwa mwa iye yekha, akhale munthu mmodzi watsopano, ndi kucitapo mtendere;

Werengani mutu wathunthu Aefeso 2

Onani Aefeso 2:15 nkhani