Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aefeso 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mwa Iyeyo inunso, mutamva mau a coonadi, Uthenga Wabwino wa cipulumutso canu; ndi kumkhulupirira iye, munasindikizidwa cizindikilo ndi Mzimu Woyera wa lonjezano,

Werengani mutu wathunthu Aefeso 1

Onani Aefeso 1:13 nkhani