Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Aefeso 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu, mwa cifuniro ca Mulungu, kwa oyera mtima amene ali m'Efeso, ndi kwa iwo okhulupirika mwa Kristu Yesu:

Werengani mutu wathunthu Aefeso 1

Onani Aefeso 1:1 nkhani