Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Yohane 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano ndikupemphani, mkazi womveka inu, wosati monga kukulemberani lamulo latsopano, koma lomwelo tinali nalo kuyambira paciyambi, kuti tikondane wina ndi mnzace.

Werengani mutu wathunthu 2 Yohane 1

Onani 2 Yohane 1:5 nkhani