Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Yohane 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cisomo, cifundo, mtendere zikhale ndi ife zocokera kwa Mulungu Atate, ndi kwa Yesu Kristu Mwana wa Atate, m'coonadi ndi m'cikondi.

Werengani mutu wathunthu 2 Yohane 1

Onani 2 Yohane 1:3 nkhani