Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cotsalira wandiikira ine korona wa cilungamo, amene Ambuye, woweruza wolungama, adzandipatsa ine tsiku lijalo: ndipo si kwa ine ndekha, komatunso kwa onse amene anakonda maonekedwe ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 4

Onani 2 Timoteo 4:8 nkhani