Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 4:19-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Lankhula Priska ndi Akula, ndi banja la Onesiforo.

20. Erasto anakhalira m'Korinto; koma Trofimo ndamsiya wodwala ku Mileto.

21. 1 Tayesetsa kudza isanadze nyengo yacisanu. Akulankhula iwe Eubulo, ndi Pude, ndi Lino, ndi Klaudiya, ndi abale onse.

22. 2 Ambuye akhale ndi mzimu wako. Cisomo cikhale nanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 4