Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 2:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zimene wazimva kwa ine mwa mboni zambiri, zomwezi uikize kwa anthu okhulupirika, amene adzadziwa kuphunzitsa enanso.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 2

Onani 2 Timoteo 2:2 nkhani