Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pokumbukila cikhulupiriro cosanyenga ciri mwa iwe, cimene cinayamba kukhala mwa mbuye wako Loisi, ndi mwa mai wako Yunike, ndipo, ndakopeka mtima, mwa iwenso.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 1

Onani 2 Timoteo 1:5 nkhani