Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Timoteo 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiyamika Mulungu, amene ndimtumikira kuyambira makolo anga ndi cikumbu mtima coyera, kuti ndikumbukila iwe kosalekeza m'mapemphero anga,

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 1

Onani 2 Timoteo 1:3 nkhani