Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Petro 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ici cimodzi musaiwale, okondedwa inu, kuti tsiku limodzi likhala kwa Ambuye ngati zaka cikwi, ndi zaka cikwi ngati tsiku limodzi.

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 3

Onani 2 Petro 3:8 nkhani