Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Petro 2:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma padakhalanso pakati pa anthuwo aneneri onama, monganso padzakhala aphunzitsi onama pakati pa inu, amene adzalowa nayo m'tseri mipatuko yotayikitsa, nadzakana Ambuye amene adawagula, nadzadzitengera iwo okha citayiko cakudza msanga.

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 2

Onani 2 Petro 2:1 nkhani