Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Petro 1:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. ndi kudziwa ici poyamba, kuti palibe cinenero ca lembo citanthauzidwa pa cokha,

21. pakuti kale lonse cinenero sicinadza ndi cifuniro ca munthu; koma anthu a Mulungu, ogwidwa ndi Mzimu Woyera, analankhula.

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1