Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Petro 1:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti analandira kwa Mulungu Atate ulemu ndi ulemerero, pakumdzera iye mao otere ocokera ku ulemerero waukuru, Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene Ine ndikondwera naye;

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1

Onani 2 Petro 1:17 nkhani