Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Petro 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

SIMONI Petro, kapolo ndi mtumwi wa Yesu Kristu kwa iwo amene adalandira cikhulupiriro ca mtengo wace womwewo ndi ife, m'cilungamo ca Mulungu wathu ndi Mpulumutsi Yesu Kristu:

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1

Onani 2 Petro 1:1 nkhani