Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Atesalonika 1:11-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Kukatero tikupemphereraninso nthawi zonse, kuti Mulungu wathu akakuyeseni inu oyenera kuitanidwa kwanu, nakakwaniritse comkomera conse, ndi nchito ya cikhulupiriro mumphamvu;

12. kuti dzina la Ambuye wathu Yesu lilemekezedwe mwa inu, ndi inu mwa iye, monga mwa cisomo ca Mulungu wathu ndi Ambuye Yesu Kristu.

Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 1