Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndinayesa kuti kufunika kupempha abale kuti atsogole afike kwa inu, nakonzeretu dalitso lanu lolonjezeka kale, kuti cikhale cokonzeka comweci, monga ngati mdalitso, ndipo si monga mwa kuumiriza.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 9

Onani 2 Akorinto 9:5 nkhani