Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace ndingakhale ndalembera kwa inu, sindinacita cifukwa ca iye amene anacita coipa, kapena cifukwa ca iye amene anacitidwa coipa, koma kuti khama lanu la kwa ife lionetsedwe kwa inu pamaso pa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 7

Onani 2 Akorinto 7:12 nkhani