Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ife tonse tiyenera kuonetsedwa ku mpando wa kuweruza wa Kristu, kuti yense alandire zocitika m'thupi, monga momwe anacita, kapena cabwino kapena coipa.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 5

Onani 2 Akorinto 5:10 nkhani