Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 3:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Koma pamene akatembenukira kwa Mulungu, cophimbaco cieotsedwa.

17. Koma Ambuye ndiye Mzimuyo; ndipo pamene pali Mzimu wa Ambuye pali ufulu.

18. Koma ife tonse ndi nkhope yosaphimbika popenyerera monga mwa kalirole ulemerero wa Ambuye, tisandulika m'cithunzihunzi comweci kucokera kuulenerero kumka kuulemerero, monga ngati kucokera kwa Ambuye Mzimu.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 3