Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinanena kale, ndipo ndinena ndisanafikeko, monga pamene ndinali pomwepo kaciwiri kaja, pokhala ine palibe, kwa iwo adacimwa kale ndi kwa onse otsala, kuti, ngati ndidzanso sindidzawaleka;

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 13

Onani 2 Akorinto 13:2 nkhani