Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 10:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi mupenyera zopenyeka pamaso? Ngati wina alimbika mwa yekha kuti ali wa Kristu, ayesere icinso mwa iye yekha, kuti monga iye ali wa Kristu, koteronso ife.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:7 nkhani