Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 10:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti sitilimba mtima kudziwerenga, kapena kudzilinganiza tokha ndi ena a iwo amene adzibvomeretsa okha; koma iwowa, podziyesera okha ndi iwo okha, ndi kudzilinganiza okha ndi iwookha, alibe nzeru.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:12 nkhani