Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ine ndekha Paulo, ndidandaulira inu mwa kufatsa ndi ulere wa Kristu, ine amene pamaso panu ndikhala wodzicepetsa pakati pa inu, koma pokhala kwina ine ndilimbika mtima kwa inu;

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 10

Onani 2 Akorinto 10:1 nkhani