Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Akorinto 1:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Si kuti ticita ufumu pa cikhulupiriro canu, koma tikhala othandizana naco cimwemwe canu; pakuti ndi cikhulupiriro muimadi.

Werengani mutu wathunthu 2 Akorinto 1

Onani 2 Akorinto 1:24 nkhani